Wikidata:Main Page/Welcome/ny

This page is a translated version of the page Wikidata:Main Page/Welcome and the translation is 100% complete.

Wikidata ndi maziko omasuka omwe angathe kuwerenga ndi kusinthidwa ndi anthu ndi makina.

Wikidata imakhala yosungirako 'deta yolongosoka za Wikimedia ndi ntchito za alongo kuphatikizapo Wikipedia, Wikivoyage, Wikisource, ndi ena.

Wikidata imaperekanso chithandizo ku malo ena ndi mautumiki kunja kwa Project Wikimedia chabe! Zomwe zili mu Wikidata zili pansi chilolezo chaulere,kutumizidwa pogwiritsa ntchito mawonekedwe oyenerera, ndipo ikhoza kusokonezedwa ku ma seti ena osatsegulidwa pa intaneti.